Bwanamkubwa wa boma la Zomba, Smart Gwedemula wati boma la Zomba lakonzeka kuchititsa chisankho cha President lachiwiri likudzali.

Read full story